Mateyu 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Inu mumachititsa kuti mtengo ndi zipatso zake zikhale zabwino kapena mumachititsa kuti mtengo ndi zipatso zake zikhale zovunda, chifukwa mtengo umadziwika ndi zipatso zake.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:33 Yesu—Ndi Njira, tsa. 104 Nsanja ya Olonda,8/15/1987, tsa. 8
33 Inu mumachititsa kuti mtengo ndi zipatso zake zikhale zabwino kapena mumachititsa kuti mtengo ndi zipatso zake zikhale zovunda, chifukwa mtengo umadziwika ndi zipatso zake.+