Mateyu 12:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndikukuuzani kuti pa Tsiku la Chiweruzo, anthu adzayankha mlandu+ pa mawu aliwonse opanda pake amene iwo amalankhula. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:36 Yesu—Ndi Njira, tsa. 104
36 Ndikukuuzani kuti pa Tsiku la Chiweruzo, anthu adzayankha mlandu+ pa mawu aliwonse opanda pake amene iwo amalankhula.