-
Mateyu 12:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Chifukwa ndi mawu ako udzaweruzidwa kuti ndiwe wolungama ndipo ndi mawu akonso udzaweruzidwa kuti ndiwe wolakwa.”
-