Mateyu 12:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Mzimu wonyansa ukatuluka mwa munthu, umadutsa mʼmalo opanda madzi kufunafuna malo okhala ndipo supeza aliwonse.+
43 Mzimu wonyansa ukatuluka mwa munthu, umadutsa mʼmalo opanda madzi kufunafuna malo okhala ndipo supeza aliwonse.+