-
Mateyu 12:44Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
44 Ndiyeno umati, ‘Ndibwerera kunyumba yanga imene ndinatulukamo ija.’ Ukafika umapeza kuti simukukhala aliyense koma ndi mosesedwa bwino komanso mokongoletsedwa.
-