Mateyu 12:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ukatero umapita kukatenga mizimu ina 7 yoipa kwambiri kuposa umenewo ndipo ikalowa mkatimo imakhala mmenemo. Zotsatira zake, zochita za munthuyo zimakhala zoipa kwambiri kuposa poyamba.+ Ndi mmenenso zidzakhalire ndi mʼbadwo woipawu.” Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:45 Yesu—Ndi Njira, tsa. 105 Nsanja ya Olonda,11/1/1995, tsa. 138/15/1987, tsa. 8
45 Ukatero umapita kukatenga mizimu ina 7 yoipa kwambiri kuposa umenewo ndipo ikalowa mkatimo imakhala mmenemo. Zotsatira zake, zochita za munthuyo zimakhala zoipa kwambiri kuposa poyamba.+ Ndi mmenenso zidzakhalire ndi mʼbadwo woipawu.”