Mateyu 12:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ali mkati molankhula ndi gulu la anthulo, kunabwera mayi ake ndi azichimwene ake.+ Iwo anaima panja ndipo ankafuna kuti alankhule naye.+
46 Ali mkati molankhula ndi gulu la anthulo, kunabwera mayi ake ndi azichimwene ake.+ Iwo anaima panja ndipo ankafuna kuti alankhule naye.+