Mateyu 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako anawauza zinthu zambiri pogwiritsa ntchito mafanizo+ kuti: “Tamverani! Wofesa mbewu anapita kukafesa mbewu.+
3 Kenako anawauza zinthu zambiri pogwiritsa ntchito mafanizo+ kuti: “Tamverani! Wofesa mbewu anapita kukafesa mbewu.+