Mateyu 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamene ankafesa, mbewu zina zinagwera mʼmbali mwa msewu ndipo kunabwera mbalame nʼkuzidya.+