Mateyu 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nʼchifukwa chake ndikulankhula nawo pogwiritsa ntchito mafanizo. Chifukwa ngakhale kuti akuyangʼana, sakuona chilichonse. Ngakhale kuti akumva, sakumvetsa zimene zikunenedwa ndipo sakuzindikira tanthauzo lake.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:13 Nsanja ya Olonda,4/1/1987, tsa. 8
13 Nʼchifukwa chake ndikulankhula nawo pogwiritsa ntchito mafanizo. Chifukwa ngakhale kuti akuyangʼana, sakuona chilichonse. Ngakhale kuti akumva, sakumvetsa zimene zikunenedwa ndipo sakuzindikira tanthauzo lake.+