Mateyu 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Munthu aliyense akamva mawu a Ufumu koma osazindikira tanthauzo lake, woipayo+ amabwera nʼkuchotsa zimene zafesedwa mumtima wa munthuyo. Iyi ndi mbewu imene inafesedwa mʼmbali mwa msewu ija.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:19 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 78-80 Nsanja ya Olonda,2/1/2003, ptsa. 8-98/1/1993, tsa. 19
19 Munthu aliyense akamva mawu a Ufumu koma osazindikira tanthauzo lake, woipayo+ amabwera nʼkuchotsa zimene zafesedwa mumtima wa munthuyo. Iyi ndi mbewu imene inafesedwa mʼmbali mwa msewu ija.+
13:19 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 78-80 Nsanja ya Olonda,2/1/2003, ptsa. 8-98/1/1993, tsa. 19