Mateyu 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma imene inafesedwa pamiyala, ndi munthu amene wamva mawu nʼkuwavomereza mwamsanga ndiponso mosangalala.+
20 Koma imene inafesedwa pamiyala, ndi munthu amene wamva mawu nʼkuwavomereza mwamsanga ndiponso mosangalala.+