-
Mateyu 13:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Komabe chifukwa chakuti amakhala alibe mizu amapitiriza kukula kwa nthawi yochepa. Koma akakumana ndi masautso kapena kuyamba kuzunzidwa chifukwa cha mawuwo, iye amapunthwa mwamsanga.
-