-
Mateyu 13:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Ndiyeno akapolo a mwinimunda uja anabwera nʼkudzamuuza kuti, ‘Ambuye, kodi mʼmesa munafesa mbewu zabwino mʼmunda mwanu? Nanga namsongole wachokeranso kuti?’
-