Mateyu 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu analankhula zonsezi ndi gulu la anthulo pogwiritsa ntchito mafanizo. Ndithudi, nthawi zonse iye ankalankhula nawo pogwiritsa ntchito mafanizo,+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:34 Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 119/1/2002, ptsa. 13-18
34 Yesu analankhula zonsezi ndi gulu la anthulo pogwiritsa ntchito mafanizo. Ndithudi, nthawi zonse iye ankalankhula nawo pogwiritsa ntchito mafanizo,+