Mateyu 13:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Mofanana ndi namsongole amene amamusonkhanitsa nʼkumuwotcha pamoto, zidzakhalanso choncho pamapeto a nthawi* ino.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:40 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2140 Nsanja ya Olonda,3/15/2010, ptsa. 22-23
40 Mofanana ndi namsongole amene amamusonkhanitsa nʼkumuwotcha pamoto, zidzakhalanso choncho pamapeto a nthawi* ino.+