Mateyu 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndipo anauza atumiki ake kuti: “Ameneyu ndi Yohane Mʼbatizi. Anauka kwa akufa ndiye nʼchifukwa chake akuchita ntchito zamphamvu.”+
2 ndipo anauza atumiki ake kuti: “Ameneyu ndi Yohane Mʼbatizi. Anauka kwa akufa ndiye nʼchifukwa chake akuchita ntchito zamphamvu.”+