Mateyu 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anachita zimenezi chifukwa Yohane ankamuuza kuti: “Nʼzosaloleka kuti mutenge mkazi ameneyu kukhala mkazi wanu.”+
4 Anachita zimenezi chifukwa Yohane ankamuuza kuti: “Nʼzosaloleka kuti mutenge mkazi ameneyu kukhala mkazi wanu.”+