Mateyu 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komabe, ngakhale kuti Herode ankafuna kupha Yohane, ankaopa gulu la anthu chifukwa iwo ankakhulupirira kuti anali mneneri.+
5 Komabe, ngakhale kuti Herode ankafuna kupha Yohane, ankaopa gulu la anthu chifukwa iwo ankakhulupirira kuti anali mneneri.+