Mateyu 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma tsiku lokumbukira kubadwa kwa Herode+ litafika, mwana wamkazi wa Herodiya anavina pa tsikulo ndipo anasangalatsa kwambiri Herode,+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:6 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 44 Nsanja ya Olonda,10/15/1998, tsa. 31
6 Koma tsiku lokumbukira kubadwa kwa Herode+ litafika, mwana wamkazi wa Herodiya anavina pa tsikulo ndipo anasangalatsa kwambiri Herode,+