Mateyu 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno mtsikanayo, mayi ake atachita kumuuza zoti apemphe ananena kuti: “Mundipatse mutu wa Yohane Mʼbatizi mʼmbale pompano.”+
8 Ndiyeno mtsikanayo, mayi ake atachita kumuuza zoti apemphe ananena kuti: “Mundipatse mutu wa Yohane Mʼbatizi mʼmbale pompano.”+