-
Mateyu 14:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Mfumuyo inamva chisoni koma poganizira lumbiro limene inapanga lija komanso anthu amene anali nawo paphwandolo, analamula kuti mutuwo uperekedwe.
-