-
Mateyu 14:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Pambuyo pake ophunzira ake anabwera kudzatenga mtembo wake nʼkukauika mʼmanda. Kenako anapita kukauza Yesu.