Mateyu 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yesu atamva zimenezi, anachoka kumeneko pangalawa nʼkupita kumalo kopanda anthu kuti akakhale payekha. Koma gulu la anthu litamva zimenezo, linamutsatira wapansi kuchokera mʼmizinda yawo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:13 Yesu—Ndi Njira, tsa. 128 Nsanja ya Olonda,9/1/1987, tsa. 16
13 Yesu atamva zimenezi, anachoka kumeneko pangalawa nʼkupita kumalo kopanda anthu kuti akakhale payekha. Koma gulu la anthu litamva zimenezo, linamutsatira wapansi kuchokera mʼmizinda yawo.+