Mateyu 14:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pa nthawiyi nʼkuti ngalawa ija itapita kutali* pakati pa madzi, ndipo inkakankhidwa mwamphamvu ndi mafunde chifukwa ankalimbana ndi mphepo yamphamvu.
24 Pa nthawiyi nʼkuti ngalawa ija itapita kutali* pakati pa madzi, ndipo inkakankhidwa mwamphamvu ndi mafunde chifukwa ankalimbana ndi mphepo yamphamvu.