-
Mateyu 14:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Ophunzirawo atamuona akuyenda panyanjapo, anachita mantha nʼkunena kuti: “Amenewa ndi masomphenya ndithu!” Ndipo anafuula mwamantha.
-