-
Mateyu 14:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Koma ataona mphepo yamkuntho, anachita mantha. Atayamba kumira anafuula kuti: “Ambuye, ndipulumutseni!”