Mateyu 14:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anthu ankamupempha kuti angogwira ulusi wopota wamʼmphepete mwa malaya ake akunja,+ ndipo anthu onse amene anaugwira anachiriratu.
36 Anthu ankamupempha kuti angogwira ulusi wopota wamʼmphepete mwa malaya ake akunja,+ ndipo anthu onse amene anaugwira anachiriratu.