Mateyu 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma iye anawayankha kuti: “Nʼchifukwa chiyani inuyo mumaphwanya malamulo a Mulungu chifukwa cha miyambo yanu?+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:3 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, tsa. 2812/1/1988, ptsa. 4-5
3 Koma iye anawayankha kuti: “Nʼchifukwa chiyani inuyo mumaphwanya malamulo a Mulungu chifukwa cha miyambo yanu?+