Mateyu 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno ophunzira ake anabwera nʼkumufunsa kuti: “Kodi mukudziwa kuti Afarisi akhumudwa ndi zimene mwanena zija?”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:12 Yesu—Ndi Njira, tsa. 136 Nsanja ya Olonda,4/1/1995, tsa. 2711/1/1987, tsa. 9
12 Ndiyeno ophunzira ake anabwera nʼkumufunsa kuti: “Kodi mukudziwa kuti Afarisi akhumudwa ndi zimene mwanena zija?”+