Mateyu 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Asiyeni amenewo. Iwo ndi atsogoleri akhungu. Choncho ngati munthu wakhungu akutsogolera wakhungu mnzake, onse awiri adzagwera mʼdzenje.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:14 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 58 Nsanja ya Olonda,4/1/1995, ptsa. 27-28
14 Asiyeni amenewo. Iwo ndi atsogoleri akhungu. Choncho ngati munthu wakhungu akutsogolera wakhungu mnzake, onse awiri adzagwera mʼdzenje.”+