Mateyu 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno kunabwera mayi wina wa ku Foinike kuchokera mʼzigawo zimenezo ndipo anafuula kuti: “Ndichitireni chifundo Ambuye, Mwana wa Davide. Mwana wanga wamkazi anagwidwa ndi chiwanda chimene chikumuzunza mwankhanza.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:22 Yesu—Ndi Njira, tsa. 138 Nsanja ya Olonda,7/1/1997, ptsa. 4-511/15/1987, tsa. 8
22 Ndiyeno kunabwera mayi wina wa ku Foinike kuchokera mʼzigawo zimenezo ndipo anafuula kuti: “Ndichitireni chifundo Ambuye, Mwana wa Davide. Mwana wanga wamkazi anagwidwa ndi chiwanda chimene chikumuzunza mwankhanza.”+