Mateyu 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yesu atachoka kumeneko, anapita kufupi ndi nyanja ya Galileya+ ndipo anakwera phiri nʼkukakhala pansi mʼphirimo. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:29 Yesu—Ndi Njira, tsa. 138 Nsanja ya Olonda,11/15/1987, tsa. 9
29 Yesu atachoka kumeneko, anapita kufupi ndi nyanja ya Galileya+ ndipo anakwera phiri nʼkukakhala pansi mʼphirimo.