Mateyu 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma Yesu anaitana ophunzira ake nʼkuwauza kuti: “Gulu la anthuli likundimvetsa chisoni,+ chifukwa anthuwa akhala ndi ine kwa masiku atatu ndipo alibe chakudya. Sindikufuna kuwauza kuti azipita ndi njala* chifukwa angalenguke panjira.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:32 “Wotsatira Wanga,” tsa. 155
32 Koma Yesu anaitana ophunzira ake nʼkuwauza kuti: “Gulu la anthuli likundimvetsa chisoni,+ chifukwa anthuwa akhala ndi ine kwa masiku atatu ndipo alibe chakudya. Sindikufuna kuwauza kuti azipita ndi njala* chifukwa angalenguke panjira.”+