Mateyu 15:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 anatenga mitanda 7 ya mkate ija ndi nsomba zija. Atayamika, anainyemanyema nʼkuyamba kupereka kwa ophunzirawo ndipo iwo anagawira gulu la anthulo.+
36 anatenga mitanda 7 ya mkate ija ndi nsomba zija. Atayamika, anainyemanyema nʼkuyamba kupereka kwa ophunzirawo ndipo iwo anagawira gulu la anthulo.+