Mateyu 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Afarisi ndi Asaduki anafika kwa Yesu ndipo pofuna kumuyesa, anamupempha kuti awaonetse chizindikiro chochokera kumwamba.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:1 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2021, tsa. 4 Nsanja ya Olonda,7/15/1993, tsa. 32
16 Kenako Afarisi ndi Asaduki anafika kwa Yesu ndipo pofuna kumuyesa, anamupempha kuti awaonetse chizindikiro chochokera kumwamba.+