-
Mateyu 16:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Koma mʼmawa mumanena kuti, ‘Lero kukuoneka kuti kugwa mvula, chifukwa kumwamba kwafiira ndipo kuli mitambo.’ Mumadziwa kumasulira kaonekedwe ka kumwamba, koma mukulephera kumasulira zizindikiro za nthawi ino.
-