Mateyu 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mʼbadwo woipa komanso wachigololo* ukufunitsitsabe chizindikiro, koma sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse+ kupatulapo chizindikiro cha Yona chokha.”+ Atanena zimenezi, anachoka nʼkuwasiya. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:4 Nsanja ya Olonda,11/1/1995, tsa. 137/15/1993, tsa. 32
4 Mʼbadwo woipa komanso wachigololo* ukufunitsitsabe chizindikiro, koma sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse+ kupatulapo chizindikiro cha Yona chokha.”+ Atanena zimenezi, anachoka nʼkuwasiya.