Mateyu 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo anayankha kuti: “Ena akumanena kuti ndinu Yohane Mʼbatizi,+ ena akumati Eliya,+ koma ena akumanena kuti Yeremiya kapena mmodzi wa aneneri.” Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:14 Yesu—Ndi Njira, tsa. 142 Yeremiya, tsa. 32 Nsanja ya Olonda,12/15/1987, tsa. 8
14 Iwo anayankha kuti: “Ena akumanena kuti ndinu Yohane Mʼbatizi,+ ena akumati Eliya,+ koma ena akumanena kuti Yeremiya kapena mmodzi wa aneneri.”