Mateyu 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yesu anamuuza kuti: “Ndiwe wosangalala Simoni mwana wa Yona, chifukwa si munthu* amene wakuululira zimenezi, koma Atate wanga amene ali kumwamba ndi amene wachita zimenezi.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:17 Tsanzirani, tsa. 191 Nsanja ya Olonda,1/1/2010, tsa. 26
17 Yesu anamuuza kuti: “Ndiwe wosangalala Simoni mwana wa Yona, chifukwa si munthu* amene wakuululira zimenezi, koma Atate wanga amene ali kumwamba ndi amene wachita zimenezi.+