-
Mateyu 16:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ine ndidzakupatsa makiyi a Ufumu wakumwamba. Chilichonse chimene udzamanga padziko lapansi chidzakhala chitamangidwa kale kumwamba, ndipo chilichonse chimene udzamasula padziko lapansi chidzakhala chitamasulidwa kale kumwamba.”
-