Mateyu 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno analamula ophunzirawo mwamphamvu kuti asauze aliyense kuti iye ndi Khristu.+