Mateyu 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kodi munthu angapindule chiyani ngati atapeza zinthu zonse zamʼdzikoli koma nʼkutaya moyo wake?+ Kapena kodi munthu angapereke chiyani choti asinthanitse ndi moyo wake?+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:26 Nsanja ya Olonda,10/15/2008, ptsa. 25-296/1/1995, tsa. 175/1/1987, tsa. 31
26 Kodi munthu angapindule chiyani ngati atapeza zinthu zonse zamʼdzikoli koma nʼkutaya moyo wake?+ Kapena kodi munthu angapereke chiyani choti asinthanitse ndi moyo wake?+