Mateyu 16:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chifukwa Mwana wa munthu adzabwera mu ulemerero wa Atate wake limodzi ndi angelo ake. Pa nthawi imeneyo adzapereka mphoto kwa aliyense mogwirizana ndi makhalidwe ake.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:27 Nsanja ya Olonda,5/15/1997, ptsa. 9-126/1/1993, tsa. 14
27 Chifukwa Mwana wa munthu adzabwera mu ulemerero wa Atate wake limodzi ndi angelo ake. Pa nthawi imeneyo adzapereka mphoto kwa aliyense mogwirizana ndi makhalidwe ake.+