Mateyu 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno iwo anaona kuti wasintha maonekedwe ake. Nkhope yake inawala ngati dzuwa ndipo malaya ake akunja anawala* kwambiri.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:2 Nsanja ya Olonda,5/15/1997, ptsa. 11, 12-149/15/1991, ptsa. 20-23
2 Ndiyeno iwo anaona kuti wasintha maonekedwe ake. Nkhope yake inawala ngati dzuwa ndipo malaya ake akunja anawala* kwambiri.+