-
Mateyu 17:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndiye Petulo anauza Yesu kuti: “Ambuye, zingakhale bwino ife titamakhala pano. Ngati mukufuna, ndimanga matenti atatu pano, imodzi yanu, imodzi ya Mose ndi ina ya Eliya.”
-