Mateyu 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akutsika mʼphirimo, Yesu anawalamula kuti: “Musauze wina aliyense za masomphenya amenewa mpaka Mwana wa munthu ataukitsidwa kwa akufa.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:9 Nsanja ya Olonda,4/1/2000, ptsa. 13-149/15/1991, tsa. 21
9 Akutsika mʼphirimo, Yesu anawalamula kuti: “Musauze wina aliyense za masomphenya amenewa mpaka Mwana wa munthu ataukitsidwa kwa akufa.”+