Mateyu 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yesu anayankha kuti: “Inu mʼbadwo wopanda chikhulupiriro ndi wopotoka maganizo,+ kodi ndikhala nanube mpaka liti? Ndipitirize kukupirirani mpaka liti? Bwera nayeni kuno.” Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:17 Yesu—Ndi Njira, tsa. 146 Nsanja ya Olonda,1/15/1988, tsa. 8
17 Yesu anayankha kuti: “Inu mʼbadwo wopanda chikhulupiriro ndi wopotoka maganizo,+ kodi ndikhala nanube mpaka liti? Ndipitirize kukupirirani mpaka liti? Bwera nayeni kuno.”