Mateyu 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Yesu anadzudzula chiwandacho ndipo chinatuluka. Nthawi yomweyo mnyamatayo anachira.+