-
Mateyu 17:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Kenako ophunzira anapita kwa Yesu ali kwayekha nʼkumufunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani ife tinalephera kutulutsa chiwanda chija?”
-